1 Akorinto 11:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti mwamuna sakhala wa kwa mkazi; koma mkazi wa kwa mwamuna; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti mwamuna sakhala wa kwa mkazi; koma mkazi wa kwa mwamuna; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pajatu mwamuna sadapangidwe kuchokera kwa mkazi, koma mkazi ndiye adapangidwa kuchokera kwa mwamuna. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pakuti mwamuna sachokera kwa mkazi, koma mkazi kwa mwamuna. Onani mutuwo |