1 Akorinto 11:21 - Buku Lopatulika21 pakuti pakudyaku yense ayamba watenga mgonero wake wa yekha, ndipo wina ali ndi njala, ndi wina aledzera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 pakuti pakudyaku yense athanga watenga mgonero wake wa yekha, ndipo wina ali ndi njala, ndi wina aledzera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Inu mumati mukamadya, aliyense angoyambapo kudya chakudya chakechake, kotero kuti wina amakhala ndi njala, m'menemo wina waledzera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti mukamadya, aliyense amangodzidyera zomwe anakonza. Wina amakhala ndi njala pamene wina amaledzera. Onani mutuwo |