1 Akorinto 11:16 - Buku Lopatulika16 Koma akaoneka wina ngati wotetana, tilibe makhalidwe otere, kapena ife, kapena Mpingo wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma akaoneka wina ngati wotetana, tilibe makhalidwe otere, kapena ife, kapena Mpingo wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono ngati wina afuna kutsutsapo pa zimenezi, ndingoti ife ndiponso mipingo ya Mulungu tilibe mwambo wina ai ndi womwewu basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ngati wina akufuna kutsutsapo pa zimenezi, ife ndiponso mipingo ya Mulungu tilibe machitidwe ena apadera koma ndi omwewa. Onani mutuwo |