1 Akorinto 11:15 - Buku Lopatulika15 Koma ngati mkazi aweta tsitsi, kuli ulemerero kwa iye; pakuti tsitsi lake lapatsidwa kwa iye ngati chophimba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma ngati mkazi aweta tsitsi, kuli ulemerero kwa iye; pakuti tsitsi lake lapatsidwa kwa iye ngati chophimba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 koma kuti kwa mkazi nchaulemu? Mulungu adapatsa mkazi tsitsi lalitali loti aziphimbira mutu wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 koma mkazi akakhala ndi tsitsi lalitali ndi ulemerero wake? Pakuti mkazi anapatsidwa tsitsi lalitali monga chophimba kumutu. Onani mutuwo |