1 Akorinto 11:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti monga mkazi ali wa kwa mwamuna, chomwechonso mwamuna ali mwa mkazi; koma zinthu zonse zili za kwa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti monga mkazi ali wa kwa mwamuna, chomwechonso mwamuna ali mwa mkazi; koma zinthu zonse zili za kwa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Inde mkazi adapangidwa kuchokera kwa mwamuna, komanso tsopano mwamuna amabadwa mwa mkazi. Ndipo zinthu zonse zimachokera kwa Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pakuti monga mkazi anachokera kwa mwamuna, momwemonso mwamuna anabadwa mwa mkazi. Koma zonse zichokera kwa Mulungu. Onani mutuwo |