1 Akorinto 11:13 - Buku Lopatulika13 Lingirirani mwa inu nokha: Kodi nkuyenera kuti apemphere kwa Mulungu, wosafunda mutu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Lingirirani mwa inu nokha: Kodi nkuyenera kuti apemphere kwa Mulungu, wosafunda mutu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Weruzani nokha ngati nkoyenera kuti mkazi azipembedza Mulungu osavala kanthu kumutu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Dziweruzeni. Kodi nʼchabwino kuti mkazi apemphere kwa Mulungu wopanda chophimba kumutu? Onani mutuwo |