Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 10:30 - Buku Lopatulika

30 Ngati ine ndilandirako mwachisomo, ndinenezedwa bwanji chifukwa cha ichi chimene ndiyamikapo?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ngati ine ndilandirako mwachisomo, ndinenezedwa bwanji chifukwa cha ichi chimene ndiyamikapo?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Ngati ine ndikuthokoza Mulungu chifukwa cha chakudya changa, nanga munthu angandinyoze bwanji chifukwa cha chakudya chimene ndikuchilandira mothokoza Mulungu?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Ngati ndikuyamika Mulungu chifukwa cha chakudya, nanga munthu angandinyoze bwanji pa zinthu zomwe ndayamikira nazo Mulungu?

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 10:30
4 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake musalole chabwino chanu achisinjirire.


Iye wakusamalira tsiku, alisamalira kwa Ambuye: ndipo iye wakudya, adya mwa Ambuye, pakuti ayamika Mulungu; ndipo iye wosadya, mwa Ambuye sakudya, nayamikanso Mulungu.


Kodi sindine mfulu? Kodi sindine mtumwi? Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu? Kodi simuli inu ntchito yanga mwa Ambuye?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa