1 Akorinto 10:29 - Buku Lopatulika29 Ndinena chikumbumtima, si cha iwe mwini, koma cha winayo; pakuti ufulu wanga uyesedwa ninji ndi chikumbumtima cha wina? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndinena chikumbu mtima, si cha iwe mwini, koma cha winayo; pakuti ufulu wanga uyesedwa ninji ndi chikumbu mtima cha wina? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Osati kuti iweyo ungavutike mu mtima ai, koma iye uja amene wakuuzayo. Pamenepo udzati, “Kodi ufulu wanga utsekerezedwe chifukwa munthu wina mtima wake ukumuvuta? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ndikunena za chikumbumtima cha winayo osati chanu. Tsono mungafunse kuti, nʼchifukwa chiyani ufulu wanga ukuphwanyidwa chifukwa cha chikumbumtima cha munthu wina? Onani mutuwo |