1 Akorinto 10:2 - Buku Lopatulika2 nabatizidwa onse kwa Mose, mumtambo, ndi m'nyanja, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 nabatizidwa onse kwa Mose, mumtambo, ndi m'nyanja, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Motero mumtambomo ndi m'nyanjamo onsewo adachita ngati kubatizidwa ndi kukhala amodzi ndi Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo onse anabatizidwa mwa Mose mu mtambo ndi mʼnyanja. Onani mutuwo |