Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 1:15 - Buku Lopatulika

15 kuti anganene mmodzi kuti mwabatizidwa m'dzina langa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 kuti anganene mmodzi kuti mwabatizidwa m'dzina langa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Motero palibe amene anganene kuti adabatizidwa m'dzina langa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 mwakuti palibe amene anganene kuti anabatizidwa mʼdzina langa.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 1:15
7 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake mukani, phunzitsani anthu a mitundu yonse, ndi kuwabatiza iwo m'dzina la Atate, ndi la Mwana, ndi la Mzimu Woyera:


nabatizidwa ndi iye mu mtsinjewo wa Yordani, alikuwulula machimo ao.


Iye wolankhula zochokera kwa iye yekha afuna ulemu wa mwini yekha. Iye wakufuna ulemu wa Iye amene anamtuma, yemweyu ali woona, ndipo mwa Iye mulibe chosalungama.


Ndiyamika Mulungu kuti sindinabatize mmodzi yense wa inu, koma Krispo ndi Gayo;


Koma ndinabatizanso a pa banja la Stefanasi; za ena, sindidziwa ngati ndinabatiza wina yense.


Pakuti ndichita nsanje pa inu ndi nsanje ya Mulungu; pakuti ndinakupalitsani ubwenzi mwamuna mmodzi, kuti ndikalangize inu ngati namwali woyera mtima kwa Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa