1 Akorinto 1:16 - Buku Lopatulika16 Koma ndinabatizanso a pa banja la Stefanasi; za ena, sindidziwa ngati ndinabatiza wina yense. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma ndinabatizanso a pa banja la Stefanasi; za ena, sindidziwa ngati ndinabatiza wina yense. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Inde ndidabatizanso Stefanasi ndi a m'banja mwake, koma sindikumbukira kuti pali winanso amene ndidamubatiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 (Inde, ine ndinabatizanso a mʼbanja la Stefano, koma sindikumbukira ngati ndinabatizanso wina aliyense). Onani mutuwo |