1 Akorinto 1:14 - Buku Lopatulika14 Ndiyamika Mulungu kuti sindinabatize mmodzi yense wa inu, koma Krispo ndi Gayo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndiyamika Mulungu kuti sindinabatiza mmodzi yense wa inu, koma Krispo ndi Gayo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ndimayamika Mulungu kuti pakati panupo sindidabatize wina aliyense, kupatula Krispo ndi Gayo basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ine ndikuyamika kuti sindinabatizepo mmodzi mwa inu kupatula Krispo ndi Gayo, Onani mutuwo |