1 Akorinto 1:13 - Buku Lopatulika13 Kodi Khristu wagawika? Kodi Paulo anapachikidwa chifukwa cha inu? Kapena kodi munabatizidwa m'dzina la Paulo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Kodi Khristu wagawika? Kodi Paulo anapachikidwa chifukwa cha inu? Kapena kodi munabatizidwa m'dzina la Paulo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Kodi Khristu wagaŵika? Kodi adakuferani pa mtanda ndi Paulo? Kodi mudabatizidwa m'dzina la Paulo? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kodi Khristu wagawikana? Kodi Paulo anapachikidwa pa mtanda chifukwa cha inu? Kodi munabatizidwa mʼdzina la Paulo? Onani mutuwo |