Ndipo pa kubadwa kwake kwa Yesu mu Betelehemu wa Yudeya m'masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum'mawa anafika ku Yerusalemu,
Yohane 11:7 - Buku Lopatulika Ndipo pambuyo pake ananena kwa ophunzira ake, Tiyeni tipitenso ku Yudeya. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pambuyo pake ananena kwa ophunzira ake, Tiyeni tipitenso ku Yudeya. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake adauza ophunzira ake kuti, “Tiyeni tipitenso ku Yudeya.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka anati kwa ophunzira ake, “Tiyeni tibwerere ku Yudeya.” |
Ndipo pa kubadwa kwake kwa Yesu mu Betelehemu wa Yudeya m'masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum'mawa anafika ku Yerusalemu,
Ndipo panali, pamene anayamba kukwanira masiku akuti alandiridwe Iye kumwamba, Yesu anatsimikiza kuloza nkhope yake kunka ku Yerusalemu,
Chifukwa chake pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pamalo pomwepo masiku awiri.
Patapita masiku, Paulo anati kwa Barnabasi, Tibwerere, tizonde abale m'mizinda yonse m'mene tinalalikiramo mau a Ambuye, tione mkhalidwe wao.