Yohane 1:2 - Buku Lopatulika Awa anali pachiyambi kwa Mulungu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Awa anali pachiyambi kwa Mulungu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anali kwa Mulungu chikhalire. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mawuwa anali ndi Mulungu pachiyambi. |
Ndinali pa mbali pake ngati mmisiri; ndinamsekeretsa tsiku ndi tsiku, ndi kukondwera pamaso pake nthawi zonse;
Ndipo ngati nditi, Sindidzamtchula Iye, sindidzanenanso m'dzina lake, pamenepo m'mtima mwanga muli ngati moto wotentha wotsekedwa m'mafupa anga, ndipo ndalema ndi kupirira, sindingathe kupiriranso.
Zonse zinalengedwa ndi Iye; ndipo kopanda Iye sikunalengedwe kanthu kalikonse kolengedwa.