Yohane 1:3 - Buku Lopatulika3 Zonse zinalengedwa ndi Iye; ndipo kopanda Iye sikunalengedwe kanthu kalikonse kolengedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Zonse zinalengedwa ndi Iye; ndipo kopanda Iye sikunalengedwa kanthu kalikonse kolengedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mulungu adalenga zonse kudzera mwa Iye, ndipo palibe chilichonse chimene chidalengedwa popanda Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Zinthu zonse zinalengedwa ndi Iye; ndipo popanda Iye sikukanakhala kanthu kalikonse kolengedwa. Onani mutuwo |