Numeri 7:78 - Buku Lopatulika Tsiku lakhumi ndi chiwiri kalonga wa ana a Nafutali, ndiye Ahira mwana wa Enani: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Tsiku lakhumi ndi chiwiri kalonga wa ana a Nafutali, ndiye Ahira mwana wa Enani: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsiku la 12 linali la Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa Anafutali, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa tsiku la khumi ndi chimodzi Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa fuko la Nafutali, anabweretsa chopereka chake. |
ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Pagiyele mwana wa Okarani.