Numeri 7:66 - Buku Lopatulika Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsiku lakhumi linali la Ahiyezere mwana wa Amishadai, mtsogoleri wa Adani. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa tsiku lakhumi Ahiyezeri mwana wa Amisadai, mtsogoleri wa fuko la Dani anabweretsa chopereka chake. |
Mbendera ya chigono cha Dani izikhala kumpoto monga mwa makamu ao; ndi kalonga wa ana a Dani ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai.