Numeri 7:5 - Buku Lopatulika Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Ulandire zimenezi kwa anthuwo kuti zithandize potumikira m'chihema chamsonkhano. Uŵapatse Alevi zimenezo, aliyense zoyenera ntchito yake.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Ulandire zimenezi kwa iwo kuti zigwire ntchito ku tenti ya msonkhano. Uzipereke kwa Alevi, aliyense monga mwa ntchito yake.” |
Okhulupirika mauwa, ndipo za izi ndifuna kuti ulimbitse mau, kuti iwo akukhulupirira Mulungu asamalire akhalebe atsogoleri a ntchito zabwino. Izi nzokoma ndi zopindulitsa anthu;