Ndipo ana a Israele anayenda ulendo wakuchokera ku Ramsesi kufikira ku Sukoti, zikwi mazana asanu ndi limodzi oyenda okha, ndiwo amuna, osawerenga ana.
Numeri 33:5 - Buku Lopatulika Ndipo ana a Israele anachokera ku Ramsesi, nayenda namanga ku Sukoti. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ana a Israele anachokera ku Ramsesi, nayenda namanga ku Sukoti. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake Aisraele adanyamuka ku Ramsesi nakamanga mahema ku Sukoti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Aisraeli atachoka ku Ramesesi, anamanga misasa yawo ku Sukoti. |
Ndipo ana a Israele anayenda ulendo wakuchokera ku Ramsesi kufikira ku Sukoti, zikwi mazana asanu ndi limodzi oyenda okha, ndiwo amuna, osawerenga ana.