ulandire masekeli asanu pa munthu mmodzi; uwalandire pa muyeso wa sekeli wa malo opatulika (sekeli ndiwo magera makumi awiri);
Numeri 3:48 - Buku Lopatulika nupereke ndalama zimene akuposawo anaomboledwa nazo kwa Aroni ndi kwa ana ake aamuna. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 nupereke ndalama zimene akuposawo anaomboledwa nazo kwa Aroni ndi kwa ana ake amuna. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Upatse Aroni pamodzi ndi ana ake aamuna ndalama zimenezi, kuti zikhale mtengo woombolera Aisraele a chiŵerengero chopitirira chija.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndalama zimenezi uzipereke kwa Aaroni ndi ana ake aamuna kuti ukhale mtengo woombolera Aisraeli woonjezerawo.” |
ulandire masekeli asanu pa munthu mmodzi; uwalandire pa muyeso wa sekeli wa malo opatulika (sekeli ndiwo magera makumi awiri);
Ndipo Mose anapatsa Aroni ndi ana ake ndalama zoombola nazo monga mwa mau a Yehova, monga Yehova adauza Mose.