Numeri 27:9 - Buku Lopatulika Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ake cholowa chake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ake cholowa chake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Akakhala kuti alibe mwana wamkazi, choloŵa chakecho chikhale cha abale ake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngati alibe mwana wamkazi, muzipereka cholowa chakecho kwa abale ake. |
Ndipo unene ndi ana a Israele, ndi kuti, Akafa munthu wamwamuna wopanda mwana wamwamuna, cholowa chake achilandire mwana wake wamkazi.