Numeri 26:8 - Buku Lopatulika Mwana wamwamuna wa Palu ndiye Eliyabu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mwana wamwamuna wa Palu ndiye Eliyabu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwana wa Palu anali Eliyabu, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwana wa Palu anali Eliabu, |
Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu.
Ndi ana a Eliyabu: Nemuwele, ndi Datani ndi Abiramu. Iwo ndiwo Datani ndi Abiramu omwe aja oitanidwa a khamu, amene anatsutsana ndi Mose ndi Aroni mu msonkhano wa Kora, muja anatsutsana ndi Yehova;