Yezere, ndiye kholo la banja la Ayezere; Silemu, ndiye kholo la banja la Asilemu.
Yezere anali kholo la banja la Ayezere. Silemu anali kholo la banja la Asilemu.
kuchokera mwa Yezeri, fuko la Ayezeri; kuchokera mwa Silemu, fuko la Asilemu.
Ndi ana aamuna a Nafutali: Yazeele, ndi Guni, ndi Yezere ndi Silemu.
Ana a Nafutali: Yaziyele, ndi Guni, ndi Yezere, ndi Salumu, ana a Biliha.