Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:24 - Buku Lopatulika

24 Ndi ana aamuna a Nafutali: Yazeele, ndi Guni, ndi Yezere ndi Silemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndi ana amuna a Nafutali: Yazeele, ndi Guni, ndi Yezere ndi Silemu

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Ana a Nafutali anali aŵa: Yazeele, Guni, Yezera ndi Silemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Ana aamuna a Nafutali ndi awa: Yahazeeli, Guni, Yezeri ndi Silemu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:24
13 Mawu Ofanana  

ana aamuna a Biliha mdzakazi wake wa Rakele: ndiwo Dani ndi Nafutali;


Ndi ana aamuna a Dani: Husimu.


Amenewa ndi ana a Biliha, amene Labani anampatsa Rakele mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo; anthu onse ndiwo asanu ndi awiri.


Nafutali ndi mbawala yomasuka; apatsa mau abwino.


Masiku a Peka mfumu ya Israele anadza Tigilati-Pilesere mfumu ya Asiriya, nalanda Iyoni, ndi Abele-Beti-Maaka, ndi Yanowa, ndi Kedesi, ndi Hazori, ndi Giliyadi, ndi Galileya, dziko lonse la Nafutali; nawatenga andende kunka nao ku Asiriya.


Ndi a Nafutali atsogoleri chikwi chimodzi, ndi pamodzi nao ogwira zikopa ndi mikondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi ziwiri.


Dani, Yosefe, ndi Benjamini, Nafutali, Gadi, ndi Asere.


Ana a Nafutali: Yaziyele, ndi Guni, ndi Yezere, ndi Salumu, ana a Biliha.


Wa Nafutali, Ahira mwana wa Enani.


Za Nafutali anati, Nafutali, wokhuta nazo zomkondweretsa, wodzala ndi mdalitso wa Yehova; landira kumadzulo ndi kumwera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa