Ndi ana aamuna a Asere: Imina, ndi Isiva, ndi Isivi, ndi Beriya, ndi Sera mlongo wao; ndi ana a Beriya: Hebere, ndi Malikiele.
Numeri 26:46 - Buku Lopatulika Ndipo dzina la mwana wamkazi wa Asere ndiye Sera. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo dzina la mwana wamkazi wa Asere ndiye Sera. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwana wamkazi wa Asere anali Sera. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero (Aseri anali ndi mwana wamkazi dzina lake Sera) |
Ndi ana aamuna a Asere: Imina, ndi Isiva, ndi Isivi, ndi Beriya, ndi Sera mlongo wao; ndi ana a Beriya: Hebere, ndi Malikiele.
Ana a Beriya ndiwo: Hebere, ndiye kholo la banja la Ahebere; Malikiele, ndiye kholo la banja la Amalikiele.
Iwo ndiwo mabanja a ana aamuna a Asere monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai.