Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Numeri 26:34 - Buku Lopatulika

Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Ameneŵa, anthu okwanira 52,700, ndiwo anali a mabanja a Manase, amene adaŵerengedwa.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Awa ndiwo anali mafuko a Manase. Amene anawerengedwa analipo 52,700.

Onani mutuwo



Numeri 26:34
4 Mawu Ofanana  

mthenga amene anandiombola ine ku zoipa zonse, adalitse anyamatawa; dzina langa litchulidwe pa iwo, ndi dzina la makolo anga Abrahamu ndi Isaki; iwo akule, nakhale khamu pakati padziko lapansi.


Ana aamuna a Efuremu monga mwa mabanja ao ndiwo: Sutela, ndiye kholo la banja la Asutela; Bekere, ndiye kholo la banja la Abekere; Tahani, ndiye kholo la banja la Atahani.