Numeri 26:24 - Buku Lopatulika Yasubu, ndiye kholo la banja la Ayasubu; Simironi, ndiye kholo la banja la Asimironi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Yasubu, ndiye kholo la banja la Ayasubu; Simironi, ndiye kholo la banja la Asimironi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yasubu anali kholo la banja la Ayasubu. Simeoni anali kholo la banja la Asimeoni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera mwa Yasubu, fuko la Ayasubu. Kuchokera mwa Simironi, fuko la Asimironi. |
Ana aamuna a Isakara monga mwa mabanja ao ndiwo: Tola, ndiye kholo la banja la Atola; Puva, ndiye kholo la banja la Apuni;
Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu.