Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:13 - Buku Lopatulika

13 Ndi ana aamuna a Isakara: Tola ndi Puva, ndi Iyobu, ndi Simironi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndi ana amuna a Isakara: Tola ndi Puva, ndi Iyobu, ndi Simironi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ana a Isakara anali aŵa: Tola, Puva, Iyobu ndi Simironi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ana aamuna a Isakara ndi awa: Tola, Puwa, Yobi ndi Simironi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:13
12 Mawu Ofanana  

ana aamuna a Leya: ndiwo Rubeni mwana woyamba wa Yakobo, ndi Simeoni ndi Levi, ndi Yuda, ndi Zebuloni, ndi Isakara;


Ndi ana aamuna a Yuda: Eri, ndi Onani, ndi Sela, ndi Perezi, ndi Zera; koma Eri ndi Onani anafa m'dziko la Kanani. Ndi ana aamuna a Perezi ndiwo Hezironi ndi Hamuli.


Ndi ana aamuna a Zebuloni: Seredi, ndi Eloni ndi Yaleele.


Ndi a ana a Isakara, anthu akuzindikira nyengo, akudziwa zoyenera Israele kuzichita, akulu ao ndiwo mazana awiri; ndi abale ao onse anapenyerera pakamwa pao.


Ana a Israele ndi awa: Rubeni, Simeoni, Levi, ndi Yuda, Isakara, ndi Zebuloni,


Wa Isakara, Netanele mwana wa Zuwara.


Ndi za Zebuloni anati, Kondwera, Zebuloni, ndi kutuluka kwako; ndi Isakara, m'mahema mwako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa