Iwo ndiwo mabanja a ana a Gadi, monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi anai ndi mazana asanu.
Ameneŵa, anthu okwanira 40,500, ndiwo anali a m'mabanja a Gadi, amene adaŵerengedwa.
Awa ndiwo anali mafuko a Gadi. Onse amene anawerengedwa analipo 40,500.
Arodi, ndiye kholo la banja la Aarodi; Areli, ndiye kholo la banja la Aareli.