Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.
Numeri 26:17 - Buku Lopatulika Arodi, ndiye kholo la banja la Aarodi; Areli, ndiye kholo la banja la Aareli. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Arodi, ndiye kholo la banja la Aarodi; Areli, ndiye kholo la banja la Aareli. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Arodi anali kholo la banja la Aarodi. Areli anali kholo la banja la Aareli. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera mwa Arodi, fuko la Aarodi; kuchokera mwa Arieli, fuko la a Areli. |
Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.
Iwo ndiwo mabanja a ana a Gadi, monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi anai ndi mazana asanu.