Numeri 15:18 - Buku Lopatulika Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene mulowa m'dziko limene ndilikukulowetsani, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene mulowa m'dziko limene ndilikukulowetsani, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Uza Aisraele kuti, ‘Mukadzaloŵa m'dziko m'mene ndidzakufikitsani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Yankhula ndi Aisraeli ndipo unene kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukutengeraniko |
Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mukakalowa m'dziko lokakhalamo inu, limene ndilikupatsa inu,
Ndipo ngati zipatso zoyamba zili zopatulika, choteronso mtanda; ndipo ngati muzu uli wopatulika, choteronso nthambi.