Numeri 15:2 - Buku Lopatulika2 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mukakalowa m'dziko lokakhalamo inu, limene ndilikupatsa inu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mukakalowa m'dziko lokakhalamo inu, limene ndilikupatsa inu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Uza Aisraele kuti, ‘Mukadzaloŵa m'dziko limene ndidzakupatsenilo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Yankhula ndi Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupatsanilo, Onani mutuwo |