Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 15:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Yankhula ndi Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupatsanilo,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mukakalowa m'dziko lokakhalamo inu, limene ndilikupatsa inu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mukakalowa m'dziko lokakhalamo inu, limene ndilikupatsa inu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Uza Aisraele kuti, ‘Mukadzaloŵa m'dziko limene ndidzakupatsenilo,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 15:2
8 Mawu Ofanana  

Mukakalowa mʼdziko la Kanaani limene ndikukupatsani kuti likhale lanu, ndipo Ine ndikakabweretsa ndere zoyanga mʼnyumba mʼdziko limenelo,


“Yankhula ndi Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupatsanilo ndi kukolola za mʼminda mwanu, mudzabwere kwa wansembe ndi mtolo wa tirigu woyambirira kucha wa mʼminda mwanu.


“Yankhula ndi Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Mukadzalowa mʼdziko limene ndikukupatsani, nthakayo iyenera kumakasunga Sabata la Yehova.


Yehova anawuza Mose kuti,


“Yankhula ndi Aisraeli ndipo unene kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukutengeraniko


Awa ndi malangizo ndi malamulo amene muyenera kusamalitsanso kuti muwatsatire mʼdziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu wakupatsani kuti mutenge pa nthawi yonse imene muti mudzakhale mʼdzikomo.


pakuti simunafike ku malo opumulirako ndi ku cholowa chimene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa