Ndipo anadza ku chigwa cha Esikolo, nachekako tsango limodzi la mphesa, nalisenza awiri mopika; anabwera nazonso makangaza ndi nkhuyu.
Numeri 13:24 - Buku Lopatulika Malowa anawatcha chigwa cha Esikolo, chifukwa cha tsangolo ana a Israele analichekako. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Malowa anawatcha chigwa cha Esikolo, chifukwa cha tsangolo ana a Israele analichekako. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Malowo adaŵatcha chigwa cha Esikolo, chifukwa cha tsango lamphesa limene anthu aja adathyola kumeneko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Malo amenewo anawatcha chigwa cha Esikolo chifukwa cha phava la mphesa limene Aisraeli anadula kumeneko. |
Ndipo anadza ku chigwa cha Esikolo, nachekako tsango limodzi la mphesa, nalisenza awiri mopika; anabwera nazonso makangaza ndi nkhuyu.
Popeza atakwera kunka ku chigwa cha Esikolo, naona dziko, anafoketsa mtima wa ana a Israele, kuti asalowe dzikoli Yehova adawapatsa.