Muombe lipenga mu Ziyoni, nimufuulitse m'phiri langa lopatulika; onse okhala m'dziko anjenjemere; pakuti tsiku la Yehova lilinkudza, pakuti liyandikira;
Numeri 10:7 - Buku Lopatulika Pomemeza msonkhano mulize, wosati chokweza ai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pomemeza msonkhano mulize, wosati chokweza ai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene mpingo wonse uyenera kusonkhana pamodzi, mulize lipenga, koma musalize lipenga lochenjeza. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pofuna kusonkhanitsa anthu, muziliza malipenga, koma mosiyana ndi mmene malipenga ochenjeza amalizidwira. |
Muombe lipenga mu Ziyoni, nimufuulitse m'phiri langa lopatulika; onse okhala m'dziko anjenjemere; pakuti tsiku la Yehova lilinkudza, pakuti liyandikira;
Ana aamuna a Aroni, ansembe, ndiwo aziliza malipenga; ndipo akhale kwa inu lemba losatha ku mibadwo yanu.