Numeri 10:24 - Buku Lopatulika Ndi pa gulu la fuko la ana a Benjamini anayang'anira Abidani mwana wa Gideoni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa gulu la fuko la ana a Benjamini anayang'anira Abidani mwana wa Gideoni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa fuko la Abenjamini anali Abidani mwana wa Gideoni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Abidani mwana wa Gideoni ndiye anali mtsogoleri wa mtundu wa Benjamini. |
Pamenepo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Dani, ndiwo a m'mbuyombuyo a zigono zonse, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Ahiyezere mwana wa Amisadai.