Numeri 7:60 - Buku Lopatulika60 Tsiku lachisanu ndi chinai kalonga wa ana a Benjamini, ndiye Abidani mwana wa Gideoni: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201460 Tsiku lachisanu ndi chinai kalonga wa ana a Benjamini, ndiye Abidani mwana wa Gideoni: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa60 Tsiku lachisanu ndi chinai linali la Abidani mwana wa Gideoni, mtsogoleri wa Abenjamini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero60 Pa tsiku lachisanu ndi chinayi Abidani mwana wa Gideoni mtsogoleri wa fuko la Benjamini, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |