Numeri 10:15 - Buku Lopatulika Ndi pa gulu la fuko la ana a Isakara panali Netanele mwana wa Zuwara. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa gulu la fuko la ana a Isakara panali Netanele mwana wa Zuwara. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanele mwana wa Zuwara. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanieli mwana wa Zuwara, |
Ndipo anayamba kuyenda ambendera ya chigono cha ana a Yuda monga mwa magulu ao; woyang'anira gulu lake ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu.