Ndipo anayamba kuyenda ambendera ya chigono cha ana a Yuda monga mwa magulu ao; woyang'anira gulu lake ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu.
Numeri 10:13 - Buku Lopatulika Potero anayamba ulendo wao monga mwa mau a Yehova ndi dzanja la Mose. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Potero anayamba ulendo wao monga mwa mau a Yehova ndi dzanja la Mose. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kameneka kanali koyamba kuti Aisraele anyamuke, Chauta atalamula kudzera mwa Mose. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kameneka kanali koyamba kuti Aisraeli anyamuke monga momwe Yehova analamulira Mose. |
Ndipo anayamba kuyenda ambendera ya chigono cha ana a Yuda monga mwa magulu ao; woyang'anira gulu lake ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu.
Ndipo pokhala mtambo pamwamba pa chihema masiku pang'ono; pamenepo anakhala m'chigono monga awauza Yehova, nayendanso ulendo monga anauza Yehova.
Powauza Yehova amanga mahema, powauza Yehova ayenda ulendo; anasunga udikiro wa Yehova powauza Yehova mwa dzanja la Mose.
Yehova Mulungu wathu ananena ndi ife mu Horebu, ndi kuti Yakwanira nthawi yokhala inu m'phiri muno;