Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 10:13 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Kameneka kanali koyamba kuti Aisraeli anyamuke monga momwe Yehova analamulira Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

13 Potero anayamba ulendo wao monga mwa mau a Yehova ndi dzanja la Mose.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Potero anayamba ulendo wao monga mwa mau a Yehova ndi dzanja la Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Kameneka kanali koyamba kuti Aisraele anyamuke, Chauta atalamula kudzera mwa Mose.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:13
4 Mawu Ofanana  

Magulu a msasa wa Yuda ndiwo anayamba kunyamuka potsata mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu lawo anali Naasoni mwana wa Aminadabu.


Nthawi zina mtambowo unkakhala pa chihemapo masiku owerengeka. Aisraeli ankamanga misasa molamulidwa ndi Yehova ndipo ankasamukanso molamulidwa ndi Iyeyo.


Molamulidwa ndi Yehova ankamanga misasa yawo ndipo ankasamukanso Yehova akawalamula. Ankamvera lamulo la Yehova kudzera mwa Mose.


Ku Horebu, Yehova Mulungu wathu anati kwa ife, “Mwakhalitsa pa phiri lino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa