Chomwecho, ngati inu, muli oipa, mudziwa kupatsa ana anu mphatso zabwino, kopambana kotani nanga Atate wanu wa Kumwamba adzapatsa zinthu zabwino kwa iwo akumpempha Iye?
Mateyu 7:10 - Buku Lopatulika Kapena pompempha nsomba, adzampatsa iye njoka kodi? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kapena pompempha nsomba, adzampatsa iye njoka kodi? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kapena atampempha nsomba, iye nkumupatsa njoka? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kapena ngati mwana apempha nsomba, kodi amamupatsa njoka? |
Chomwecho, ngati inu, muli oipa, mudziwa kupatsa ana anu mphatso zabwino, kopambana kotani nanga Atate wanu wa Kumwamba adzapatsa zinthu zabwino kwa iwo akumpempha Iye?
Ndipo monga Mose anakweza njoka m'chipululu, chotero Mwana wa Munthu ayenera kukwezedwa;
Koma ndiopa, kuti pena, monga njoka inanyenga Heva ndi kuchenjerera kwake, maganizo anu angaipsidwe kusiyana nako kuona mtima ndi kuyera mtima zili kwa Khristu.