Mateyu 16:5 - Buku Lopatulika Ndipo ophunzira anadza kutsidya linalo, naiwala kutenga mikate. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ophunzira anadza kutsidya linalo, naiwala kutenga mikate. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene ophunzira aja adakafika kutsidya, anali ataiŵala kutenga buledi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma atawoloka nyanja, ophunzira anayiwala kutenga buledi. |
Obadwa oipa ndi achigololo afunafuna chizindikiro; ndipo sadzalandira chizindikiro china, koma chizindikiro cha Yona. Ndipo Iye anawasiya, nachokapo.
Ndipo Yesu anati kwa iwo, Yang'anirani mupewe chotupitsa mkate cha Afarisi ndi Asaduki.