Chiritsani akudwala, ukitsani akufa, konzani akhate, tulutsani ziwanda: munalandira kwaulere, patsani kwaulere.
Mateyu 10:9 - Buku Lopatulika Musadzitengere ndalama zagolide, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Musadzitengere ndalama zagolide, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Musatenge ndalama m'zikwama, kaya nzagolide, kaya nzasiliva, kaya nzakopala. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Musatenge ndalama zagolide kapena zasiliva kapena zakopala mʼzikwama mwanu; |
Chiritsani akudwala, ukitsani akufa, konzani akhate, tulutsani ziwanda: munalandira kwaulere, patsani kwaulere.
Ndipo anadziitanira khumi ndi awiriwo, nayamba kuwatumiza iwo awiriawiri; nawapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa;
Ndipo anati kwa iwo, Pamene ndinakutumizani opanda thumba la ndalama, ndi thumba la kamba, ndi nsapato, munasowa kanthu kodi? Anati iwo, Iai.