Momwemo tsiku lakukondwera inu, ndi nyengo zoikidwa zanu, ndi poyamba miyezi yanu, muziliza malipenga pa nsembe zanu zopsereza, ndi pa nsembe zanu zoyamika; ndipo akhale kwa inu chikumbutso pamaso pa Mulungu wanu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
Masalimo 81:4 - Buku Lopatulika Pakuti ichi ndi cholemba cha kwa Israele, chiweruzo cha Mulungu wa Yakobo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti ichi ndi cholemba cha kwa Israele, chiweruzo cha Mulungu wa Yakobo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pakuti ndilo lamulo lokhalira Israele, lochokera kwa Mulungu wa Yakobe, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ili ndi lamulo kwa Israeli, langizo la Mulungu wa Yakobo. |
Momwemo tsiku lakukondwera inu, ndi nyengo zoikidwa zanu, ndi poyamba miyezi yanu, muziliza malipenga pa nsembe zanu zopsereza, ndi pa nsembe zanu zoyamika; ndipo akhale kwa inu chikumbutso pamaso pa Mulungu wanu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
Ndipo poyamba miyezi yanu muzibwera nayo nsembe yopsereza ya Yehova: ng'ombe zamphongo ziwiri, ndi nkhosa yamphongo imodzi, ndi anaankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi opanda chilema;