Nenepetsa mtima wa anthu awa, lemeretsa makutu ao, nutseke maso ao; angaone ndi maso ao, angamve ndi makutu ao, angazindikire ndi mtima wao, nakabwerenso, nachiritsidwe.
Masalimo 135:16 - Buku Lopatulika Pakamwa ali napo koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakamwa ali napo koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pakamwa ali napo, koma salankhula, maso ali nawo, koma sapenya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pakamwa ali napo koma sayankhula maso ali nawo, koma sapenya; |
Nenepetsa mtima wa anthu awa, lemeretsa makutu ao, nutseke maso ao; angaone ndi maso ao, angamve ndi makutu ao, angazindikire ndi mtima wao, nakabwerenso, nachiritsidwe.