Ndipo Israele anamkantha ndi lupanga lakuthwa, nalanda dziko lake likhale laolao, kuyambira Arinoni kufikira Yaboki, kufikira ana a Amoni; popeza malire a ana a Amoni ndiwo olimba.
Masalimo 135:10 - Buku Lopatulika Ndiye amene anapanda amitundu ambiri, napha mafumu amphamvu; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndiye amene anapanda amitundu ambiri, napha mafumu amphamvu; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndiye amene adaononga mitundu yambiri ya anthu, ndi kupha mafumu amphamvu aja, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anakantha mitundu yambiri ya anthu ndi kupha mafumu amphamvu: |
Ndipo Israele anamkantha ndi lupanga lakuthwa, nalanda dziko lake likhale laolao, kuyambira Arinoni kufikira Yaboki, kufikira ana a Amoni; popeza malire a ana a Amoni ndiwo olimba.
Ndipo anamkantha iye, ndi ana ake aamuna ndi anthu ake onse, kufikira sanatsale ndi mmodzi yense; nalanda dziko lake likhale laolao.