Pomwepo Iye anasiya makamuwo, nalowa m'nyumba; ndimo ophunzira ake anadza kwa Iye, nanena, Mutitanthauzire fanizo lija la namsongole wa m'munda.
Marko 8:9 - Buku Lopatulika Ndipo iwo anali ngati zikwi zinai; ndipo Iye analawirana nao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iwo anali ngati zikwi zinai; ndipo Iye analawirana nao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu amene adaali pamenepo, amuna okha adaalipo ngati zikwi zinai. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Panali amuna pafupifupi 4,000. Ndipo atawawuza kuti apite kwawo, |
Pomwepo Iye anasiya makamuwo, nalowa m'nyumba; ndimo ophunzira ake anadza kwa Iye, nanena, Mutitanthauzire fanizo lija la namsongole wa m'munda.
Ndipo anadzitengera khumi ndi awiriwo, nati kwa iwo, Taonani, tikwera kunka ku Yerusalemu, ndipo zidzakwaniritsidwa kwa Mwana wa Munthu zonse zolembedwa ndi aneneri.