Pakudzaonekera inu pamaso pa Ine, ndani wafuna chimenechi m'dzanja lanu, kupondaponda m'mabwalo mwanga?
Marko 7:8 - Buku Lopatulika Musiya lamulo la Mulungu, nimusunga mwambo wa anthu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Musiya lamulo la Mulungu, nimusunga mwambo wa anthu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kenaka Yesu adati, “Inu mumasiya Malamulo a Mulungu, nkumasunga miyambo ya anthu.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwasiya malamulo a Mulungu ndipo mwagwiritsitsa miyambo ya anthu.” |
Pakudzaonekera inu pamaso pa Ine, ndani wafuna chimenechi m'dzanja lanu, kupondaponda m'mabwalo mwanga?
Ndipo Afarisi ndi alembi anamfunsa Iye, kuti, Bwanji ophunzira anu satsata mwambo wa akulu, koma akudya mkate wao ndi m'manja mwakuda?
ndipo ndinawaposa ndi kutsogola mwa Chiyuda ambiri a msinkhu wanga mwa mtundu wanga, ndipo ndinakhala wachangu koposa pa miyambo ya makolo anga.