Marko 5:1 - Buku Lopatulika Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, kudziko la Agerasa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, kudziko la Agerasa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Yesu ndi ophunzira ake adafika ku tsidya la Nyanja ya Galileya, ku dera la Agerasa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo anawoloka nyanja napita ku dera la Gerasa. |
Ndipo iwo anachita mantha aakulu, nanenana wina ndi mnzake, Uyu ndani nanga, kuti ingakhale mphepo ndi nyanja zimvera Iye?